ELI NJUCHI LATEST UPDATE
- Get link
- X
- Other Apps
ELI NJUCHI IS BACK ONLINE AFTER A FEW MONTHS OFFLINE
Eli Njuchi wabweleraso paline atakhala nthawi yaitali asakulowa paline komanso kupanga deactivate ma account ake onse, Eli Njuchi anapanga nawonso perform ku Show ya Onesimus Vs Armstrong... Ndipo anthu ambiri akondwela chifukwa chakubwera kwake... Inuyo mwamulandira bwanji Eli?? Wonerani performance yake musimu👇
- Get link
- X
- Other Apps

Comments
Post a Comment