PHYZIX ANAWULURA ZAMBIRI MU NYIMBO ENA AMAONA NGATI NDI NSANJE
- Get link
- X
- Other Apps
Khwimbi la Anthu layamba kugwirizana nazo zomwe anaimba Phyzix mu Nyimbo ya These Nigaz yomwe inali Diss yopita kwa oyimba mnzake... Ambiri nthawi imeneyo ankaona ngati ndi nsanje koma pano ayamba kukhulupira chifukwa ena mwa oyimbawa atchulidwaso ndi Lawyer odziwika bwino ndikuthana ndi Katangale, kuti akukhudzidwa ndi Katangale .. onani Screenshot
- Get link
- X
- Other Apps


Comments
Post a Comment